A Chilambula alankhula izi lero atamaliza kupereka zikalata zawo zowayeneleza kudzapikisana nawo pachisankho chapa 16 September ngati mphungu pansi pa chipani cha …
July 2025
-
-
Lifestyle
Kampani ya China Civil Engineering Construction kudzera mu unduna wa za mtengatenga ndi mtokoma yapereka ma life jacket 250 ku boma la Likoma.
M’mau ake m’modzi mwa akuluakulu oyang’anila za mayendedwe apa madzi omwe achokera ku nthambi ya Marine, Captain Peter Kajadu ati thandizoli ndilofunika …
-
Politics
Yemwe adzapikisane nawo pampando wa ukhansala muwodi ya Chizumulu North m’boma la Likoma ati ndiwokonzeka kutumikila anthu akuderali.
A Andrew Zex Msalowa omwe adzayimile chipani cha Malawi Congress Party MCP, anena izi lero pa Chizumulu Community ground pomwe amakhazikitsa mfundo …
-
Featured
Kuchedwetsa ntchito kwa kontilakitara kwapangitsa kuti ntchito yomanga chipatala chaching’ono cha YoMa healthy Post m’boma la Likoma chisathe munthawi yake.
Wachiwiri kwa wapampando wakomiti yoyang’anila chitukuko kuderali yemweso ndi wapampando wa chitukuko wa Yoma VDC a Aliston Katemetcha ati kontilakita yemwe akumanga …
-
Politics
A Philip Chika Chilambula omwe anagonja pachisankho chachipulura pa mpando wa ukhansala mchipani cha Democratic Progressive Party DPP, akuti adzapikisana nawo pampandowo ngati oyima pawokha.
A Chilambula alankhula ndi Likoma radio kuti sanali okhutila ndi chisankho chomwe chinachitika mwezi wa Epulu ndipo ati anthu asamakopeke ndi ndalama …
-
Featured
Bungwe lowona za chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) litsegulira nyengo ya misonkhano yokopa anthu pa 14 July 2025, pokonzekera chisankho chomwe chidzachitike pa 16 September chaka chino.
Malingana ndi kalata yomwe bungweri ladatulutsa pa 9 Julayi ndipo wasaina ndi mneneri wa bungweri a Sangwani Mwafulirwa yati mwambo otsegulira nyengo …
-
Featured
Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwela wapempha achinyamata kuti achite machawi pofusila ndalama ya mthumba la Youth Innovation Fund.
Achakwera anena izi pamsonkhano wa achinyamata omwe ukuchitikira mu mzinda wa Lilongwe pamutu wakuti ‘Harnessing Youth Innovation for Economic Employment and Sustainable …