A Nyirongo awuza Likoma Radio kuti kupeleka katemelayu kwatengera kupezeka kwa Polio munzinda wa Blantyre kotero a zaumoyo akangalika kupeleka katemelayu komanso …
Monthly Archives
March 2026
-
-
Featured
Wamkulu wa kampani ya Malawi Lake Services wati kukweza mitengo kwa sitima ya MV Ilala kupititsa patsogolo ntchito za kampaniyi.
A Joseph Sheketani Banda alankhula izi lachinayi pamkumano omwe anakonzera atolankhani a m’boma la Likoma ndicholinga chowadziwitsa momwe kampaniyi imagwilira ntchito zake. …
-
Featured
Wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo yemwenso ndi phungu wa Likoma Islands Constituency a Charles Chilambula ati kubwera kwa incinerator m’boma la Likoma kupititsa patsogolo ntchito za umoyo.
A Chilambula anena izi lamulungu kutsatila kufika kwa incinerator yi pa chipatala cha Chima m’bomali. “Kumbuyoku tikafuna kuwotcha zinthu zina tinkazitumiza ku …