Home Politics A Philip Chika Chilambula omwe anagonja pachisankho chachipulura pa mpando wa ukhansala mchipani cha Democratic Progressive Party DPP, akuti adzapikisana nawo pampandowo ngati oyima pawokha.

A Philip Chika Chilambula omwe anagonja pachisankho chachipulura pa mpando wa ukhansala mchipani cha Democratic Progressive Party DPP, akuti adzapikisana nawo pampandowo ngati oyima pawokha.

by Chiletso Bisweck
0 comments

A Chilambula alankhula ndi Likoma radio kuti sanali okhutila ndi chisankho chomwe chinachitika mwezi wa Epulu ndipo ati anthu asamakopeke ndi ndalama koma mfundo.

“takhala tikuyenda pagalawundi ndichimene chandipatsa chitsimikizo kuti kuthekera kutha kupezeka ngati titapanga bwino kampeni”, atero a Philip.

Pakadali pano achilambula akuti chilichonse chofunika kuti adzapikisane nawo apanga kale kuphatikizapo kutenga zipepala ku ofesi ya MEC komanso kupeleka ndalama.

Zatelemu anthu okwana asanu ndiwomwe awonetsa chidwi chodzapikisana pa mpando wa ukhansala mchigawo chakumwela kwa chilumba cha Likoma.

LikomaFM, OnlineNews.

You may also like

Leave a Comment

Likoma (LCR) is a community radio for Likoma District licensed by
Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA) in December
2013.The Radio is covering the whole of Likoma District including
Chizumulu, parts of Nkhata Bay,Mzuzu and Nkhotakota. The radio
station enjoys a listenership of about 50,000 comprising of 17,000 from
the island and others from Nkhata Bay, Nkhotakota and some parts
of Mozambique.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00