Home Featured Mkulu woyang’anira nkhani za katemera wa Polio mdziko muno, a Blessing Nyirongo ati ali ndi chikhulupiliro kuti kampeni yopeleka katemera wamatendawa m’boma la Likoma ikhala yopambana.

Mkulu woyang’anira nkhani za katemera wa Polio mdziko muno, a Blessing Nyirongo ati ali ndi chikhulupiliro kuti kampeni yopeleka katemera wamatendawa m’boma la Likoma ikhala yopambana.

by Oliver Malibisa
0 comments

A Nyirongo awuza Likoma Radio kuti kupeleka katemelayu kwatengera kupezeka kwa Polio munzinda wa Blantyre kotero a zaumoyo akangalika kupeleka katemelayu komanso kufalitsa mauthenga akuopsa kwa Polio.

Polankhulapo ofalitsa nkhani zaumoyo m’bomali a Adamson Chunga ati ana omwe amalandila katemelayu amakhala otetezeka ku matendawa.

A Chunda ati pali chiyembekezo kuti ntchito yopeleka katemelayu idzayambe pa 24 mpaka pa 27 March 2026, ndipo ana 3644 osaposera zaka khumi zakubadwa ndiwomwe akuyembezeka kulandira katemelayu.

LikomaFM,OnlineNews.

You may also like

Leave a Comment

Likoma (LCR) is a community radio for Likoma District licensed by
Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA) in December
2013.The Radio is covering the whole of Likoma District including
Chizumulu, parts of Nkhata Bay,Mzuzu and Nkhotakota. The radio
station enjoys a listenership of about 50,000 comprising of 17,000 from
the island and others from Nkhata Bay, Nkhotakota and some parts
of Mozambique.

Newsletter

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00