Home Entertainment Atachita zii kwa zaka zinayi m’modzi mwa oyimba wapa chilumba cha Chizumulu, Memory Pondomali yemwe amatchuka ndi dzina lakuti Nyapondo wati akhala akutulutsa nyimbo yatsopano yomwe akuyitcha “Zani”.

Atachita zii kwa zaka zinayi m’modzi mwa oyimba wapa chilumba cha Chizumulu, Memory Pondomali yemwe amatchuka ndi dzina lakuti Nyapondo wati akhala akutulutsa nyimbo yatsopano yomwe akuyitcha “Zani”.

by Chiletso Bisweck
0 comments

Nyapondo wati nyimboyi yomwe wajambula Video komanso audio zonse zitulutsidwa pa 1 February 2026, “panopa ndikhala okhazikika chifukwa ndinawoloka zomwe zakhala zikundifowoketsa ndipo onditsatila ayembekezere nyimbo zothyakuka”.

Iye wati nyimbo yatsopanoyi yajambulidwa ndi DJ Lobodo pomwe Video wajambula ndi Twice P.

LikomaFM, OnlineNews.

Leave a Comment

Likoma (LCR) is a community radio for Likoma District licensed by
Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA) in December
2013.The Radio is covering the whole of Likoma District including
Chizumulu, parts of Nkhata Bay,Mzuzu and Nkhotakota. The radio
station enjoys a listenership of about 50,000 comprising of 17,000 from
the island and others from Nkhata Bay, Nkhotakota and some parts
of Mozambique.

Newsletter

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00