Izi zili chonchi kutsatila masewero omwe anachitika Lamulungu lapitali pa Madimba Community Ground mndime ya Semi final pakati pa Nkhwazi fc ndi …
Chiletso Bisweck
-
-
Featured
‎kutsatila kutsegulira kwa sukulu pa 22 September chaka chino, gulu la achinyamata lochokera kwa a mfumu a Mani m’mudzi wa Mbungo lapeleka makope ndi zolembera kwa ana apasukulu ya mbungo m’boma la Likoma.‎‎
M,modzi mwa achinyamata omwe apelereka makopewa a Nick Mkuyamba ati cholinga chachikulu cha gulu lawo ndikupititsa patsogolo maphunziro musukulu za primary m’bomali.‎‎Nawo …
-
Vuto lakusowa kwa madzi a ukhondo lafika posauzana pa chilumba cha chizumulu m’boma la Likoma. Polankhula ndi Likoma Radio mkulu woyang’anira sikimu …
-
Featured
Sukulu ya Likoma Sekondale yalandila galimoto ya tsopano yomwe ikhale ikuchepetsa mavuto a mayendedwe.
Polandila galimotoyi lachinayi m’phunzitsi wamkulu wa pa sukukuyi a Jeremiah Mzumala ati akuthokoza boma kudzera ku nduna yoona za maphunziro a Madalitso …
-
Sports
Mkulu woyendetsa nkhani za masewero m’boma la Likoma wati anthu okhala m’bomali ayembekezele kuona kusintha pa nkhani za masewero.
A Antonio Manda anena izi lero pamkumano omwe amakumana ndi atsogoleri oyendetsa masewero osayinasiyana m’bomali. M’mawu awo a Manda ati m’boma la …
-
Politics
A Charles Chilambula omwe adzapikisane nawo pa mpando waphungu wa nyumba yamalamulo ku Likoma ati apitiliza kuchititsa misonkhano yokopa anthu kuti adzapambane pa chisankho chapa 16 September.
A Chilambula alankhula izi lero atamaliza kupereka zikalata zawo zowayeneleza kudzapikisana nawo pachisankho chapa 16 September ngati mphungu pansi pa chipani cha …
-
Lifestyle
Kampani ya China Civil Engineering Construction kudzera mu unduna wa za mtengatenga ndi mtokoma yapereka ma life jacket 250 ku boma la Likoma.
M’mau ake m’modzi mwa akuluakulu oyang’anila za mayendedwe apa madzi omwe achokera ku nthambi ya Marine, Captain Peter Kajadu ati thandizoli ndilofunika …
-
Politics
Yemwe adzapikisane nawo pampando wa ukhansala muwodi ya Chizumulu North m’boma la Likoma ati ndiwokonzeka kutumikila anthu akuderali.
A Andrew Zex Msalowa omwe adzayimile chipani cha Malawi Congress Party MCP, anena izi lero pa Chizumulu Community ground pomwe amakhazikitsa mfundo …
-
Featured
Kuchedwetsa ntchito kwa kontilakitara kwapangitsa kuti ntchito yomanga chipatala chaching’ono cha YoMa healthy Post m’boma la Likoma chisathe munthawi yake.
Wachiwiri kwa wapampando wakomiti yoyang’anila chitukuko kuderali yemweso ndi wapampando wa chitukuko wa Yoma VDC a Aliston Katemetcha ati kontilakita yemwe akumanga …
-
Politics
A Philip Chika Chilambula omwe anagonja pachisankho chachipulura pa mpando wa ukhansala mchipani cha Democratic Progressive Party DPP, akuti adzapikisana nawo pampandowo ngati oyima pawokha.
A Chilambula alankhula ndi Likoma radio kuti sanali okhutila ndi chisankho chomwe chinachitika mwezi wa Epulu ndipo ati anthu asamakopeke ndi ndalama …