Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwanyengo yati nyengo ya Chiperoni ikuyembekezeka kuchepa mphanvu lero ndipo mawa m’madera ambiri kudzakhala kwa nyengo ya …
Featured
-
-
Featured
Pofuna kupititsa patsogolo ntchito za Maphunziro m’dziko muno, Nduna ya Maphunziro a Madalitso Kambauwa Wirima atsegulira ofesi ya aphunzitsi (TDC) pa chilumba cha Chizumulu m’boma la Likoma.
Polankhula la chiwiri pa Chilumba cha Chizumulu pamwambo otsegulira ofesiyi omwe unatsogozedwa ndi Phungu wa Likoma a Christopher Ashems Songwe, ndunayi yati …
-
Featured
Khonsolo ya Likoma yati mwayi wa ntchito zosiyanasiyana ulipo mukhonsoloyi kwa achinyamata omwe ali ndi zowayeneleza.
Poyankha funso la phungu wa Likoma a Christopher Ashems Songwe lomwe anafunsa lachisanu pa mkumano wa Full Council lokhudza ndondomeko zakalembedwe ka …
-
Featured
Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati mitambo ya mvula ya mabingu yayambapo kale kusonkhana m’madera ena am’dziko muno.
Madelawa ndi monga, Blantyre, Thyolo, Phalombe, Mangochi, Mwanza, Salima mwa ochepa chabe. Nthambiyi yati izi zikupereka chiyembekezo cha mvula ya mabingu m’maderawa …
-
Featured
Apolice M’boma la Likoma agwira abambo atatu ndikuwasunga muchitolokosi powaganizira mulandu wakuba komanso kupezeka ndi katundu wa anthu omwe anamira pangozi ya bwato yomwe inachitika loweluka sabata yapitayi m’bomali pomwe anthuwa amakakwera sitima ya MV Chilembwe.
Malingana ndi ofalitsa nkhani za Police ku Likoma sergeant Enala Kaluwa wati pawukadaulo wawo akwanitsa kugwira anthuwa ndipo onsewa akuyembekezeka kukawonekera kubwalo …
-
Featured
Sitima ya MV Chilembwe idziyenda kawiri patsiku kuyambila pa 15 April pakati pa boma la Likoma ndi Nkhata Bay.
“Ndiyankha pompano zokhudza MV Chilembwe zomwe phungu wanyumba ya malamulo wapempha”, nduna yowona za mayendedwe ndi mtengatenga a Jacob Hara ndiwo anena …
-
Featured
Opindula ndi ndondomeko ya mtukula pakhomo m’boma la Likoma ati njira yatsopano yolandila ndalama kudzera pa phone ndiyodalilika.
Izi zadziwika Likoma radio itayendera ena mwa opindula ndi ndondomekoyi pa chilumba cha Chizumulu kufuna kunva momwe opindulawa ayilandilila njila yamakonoyi yomwe …