Vuto lakusowa kwa madzi a ukhondo lafika posauzana pa chilumba cha chizumulu m’boma la Likoma. Polankhula ndi Likoma Radio mkulu woyang’anira sikimu …
Featured
-
-
Featured
Sukulu ya Likoma Sekondale yalandila galimoto ya tsopano yomwe ikhale ikuchepetsa mavuto a mayendedwe.
Polandila galimotoyi lachinayi m’phunzitsi wamkulu wa pa sukukuyi a Jeremiah Mzumala ati akuthokoza boma kudzera ku nduna yoona za maphunziro a Madalitso …
-
Featured
Kuchedwetsa ntchito kwa kontilakitara kwapangitsa kuti ntchito yomanga chipatala chaching’ono cha YoMa healthy Post m’boma la Likoma chisathe munthawi yake.
Wachiwiri kwa wapampando wakomiti yoyang’anila chitukuko kuderali yemweso ndi wapampando wa chitukuko wa Yoma VDC a Aliston Katemetcha ati kontilakita yemwe akumanga …
-
Featured
Bungwe lowona za chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) litsegulira nyengo ya misonkhano yokopa anthu pa 14 July 2025, pokonzekera chisankho chomwe chidzachitike pa 16 September chaka chino.
Malingana ndi kalata yomwe bungweri ladatulutsa pa 9 Julayi ndipo wasaina ndi mneneri wa bungweri a Sangwani Mwafulirwa yati mwambo otsegulira nyengo …
-
Featured
Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwela wapempha achinyamata kuti achite machawi pofusila ndalama ya mthumba la Youth Innovation Fund.
Achakwera anena izi pamsonkhano wa achinyamata omwe ukuchitikira mu mzinda wa Lilongwe pamutu wakuti ‘Harnessing Youth Innovation for Economic Employment and Sustainable …
-
Featured
Khonsolo ya Boma la Likoma yayamba ntchito yomanga nyumba yosungilamo katundu wa ngozi zogwa mwadzidzi.
Ntchito yomanga nyumbayi yomwe imangidwe ku Ngani pansi pa CHAKO VDC yayambika lero ndipo igwilika kwa masiku 90. M’mawu awo nkulu oyang’anila …
-
Featured
Bishop wa Anglican Dioceses of Northern Malawi wati mpingo uli ndi udindo waukulu potengapo mbali pachitukuko chadziko lino.
Rt.Rev. Fanuel Magangani wanena izi lamulungu lapitali pa St Peters Anglican Cathedral m’boma la likoma pamwambo osangalalira kuti Dioceses yi yakwanitsa zaka …
-
Featured
Pomwe dziko lino likukonzekera chisankho chapatatu bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electral Commission likupitiliza kudziwitsa adindo osiyanasiyana za ndondomeko yachisankho.
Mkulu owona zachisankho m’boma la Likoma a Theophilus Msachi lero achititsa mkumano wa mafumu ndi atsogoleli azipembedzo pofuna kuwadziwitsa za ntchito yotsimikizila …
-
Featured
Mulandu wayemwe akumuganizira kuti ndi m’modzi mwawoyendetsa Boat lomwe linachita ngozi ndikupha anthu nkhumi ndi modzi m’mawa wapa 12 April, 2025, m’boma la Likoma wayamba lero.
Malingana ndi His Worship Fordwatch Nyamazana Mkandawire wati mlanduwu ukuyembekezeka kupitilira lachisanu sabata ino. Naye otengera milandu ku bwalo lamilandu Sergeant Charles …
-
Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwanyengo yati nyengo ya Chiperoni ikuyembekezeka kuchepa mphanvu lero ndipo mawa m’madera ambiri kudzakhala kwa nyengo ya …