M,modzi mwa achinyamata omwe apelereka makopewa a Nick Mkuyamba ati cholinga chachikulu cha gulu lawo ndikupititsa patsogolo maphunziro musukulu za primary m’bomali.‎‎Nawo …
Featured
-
-
Featured
Mulandu wayemwe akumuganizira kuti ndi m’modzi mwawoyendetsa Boat lomwe linachita ngozi ndikupha anthu nkhumi ndi modzi m’mawa wapa 12 April, 2025, m’boma la Likoma wayamba lero.
Malingana ndi His Worship Fordwatch Nyamazana Mkandawire wati mlanduwu ukuyembekezeka kupitilira lachisanu sabata ino. Naye otengera milandu ku bwalo lamilandu Sergeant Charles …
-
Featured
Khonsolo ya Likoma yati mwayi wa ntchito zosiyanasiyana ulipo mukhonsoloyi kwa achinyamata omwe ali ndi zowayeneleza.
Poyankha funso la phungu wa Likoma a Christopher Ashems Songwe lomwe anafunsa lachisanu pa mkumano wa Full Council lokhudza ndondomeko zakalembedwe ka …
-
Featured
Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati mitambo ya mvula ya mabingu yayambapo kale kusonkhana m’madera ena am’dziko muno.
Madelawa ndi monga, Blantyre, Thyolo, Phalombe, Mangochi, Mwanza, Salima mwa ochepa chabe. Nthambiyi yati izi zikupereka chiyembekezo cha mvula ya mabingu m’maderawa …
-
Featured
Apolice M’boma la Likoma agwira abambo atatu ndikuwasunga muchitolokosi powaganizira mulandu wakuba komanso kupezeka ndi katundu wa anthu omwe anamira pangozi ya bwato yomwe inachitika loweluka sabata yapitayi m’bomali pomwe anthuwa amakakwera sitima ya MV Chilembwe.
Malingana ndi ofalitsa nkhani za Police ku Likoma sergeant Enala Kaluwa wati pawukadaulo wawo akwanitsa kugwira anthuwa ndipo onsewa akuyembekezeka kukawonekera kubwalo …
-
Featured
Sitima ya MV Chilembwe idziyenda kawiri patsiku kuyambila pa 15 April pakati pa boma la Likoma ndi Nkhata Bay.
“Ndiyankha pompano zokhudza MV Chilembwe zomwe phungu wanyumba ya malamulo wapempha”, nduna yowona za mayendedwe ndi mtengatenga a Jacob Hara ndiwo anena …
-
Featured
Opindula ndi ndondomeko ya mtukula pakhomo m’boma la Likoma ati njira yatsopano yolandila ndalama kudzera pa phone ndiyodalilika.
Izi zadziwika Likoma radio itayendera ena mwa opindula ndi ndondomekoyi pa chilumba cha Chizumulu kufuna kunva momwe opindulawa ayilandilila njila yamakonoyi yomwe …