A Yamikani Mwambafula awuza Likoma Radio kuti pakadali pano chilichonse chokonzekera mwambowu chilimchimake ndipo ati patsikuli anthu ayembekezere kudzasangalatsidwa ndi oyimba osiyanasiyana …
Lifestyle
-
-
Lifestyle
Kampani ya China Civil Engineering Construction kudzera mu unduna wa za mtengatenga ndi mtokoma yapereka ma life jacket 250 ku boma la Likoma.
M’mau ake m’modzi mwa akuluakulu oyang’anila za mayendedwe apa madzi omwe achokera ku nthambi ya Marine, Captain Peter Kajadu ati thandizoli ndilofunika …
-
Lifestyle
Wapampando wa khonsolo ya boma la Likoma wati anthu omwe amapindula ndi porogalamu ya mtukula pakhomo adzigwilitsa moyenera ndalama zomwe amalandila mu porogalamuyi.
A Barnabas Sambamu anena izi lamulungu pomwe khonsolo ya Likoma inakonza masewelo ampira wamiyendo ndicholinga chakuti apeleke uthenga wamomwe porogalamuyi imayendela, pamutu …
-
Lifestyle
Gulu la Tilerane la m’mudzi wa mfumu Mani M’boma la Likoma lathandiza mabanja awiri osowa ndikatundu ogonera.
Polankhula loweluka pamwambo opeleka katundu kumabanjawa, Wapampando wa Guluri mayi Gladies Njakale ati cholinga chaguluri ndikuonetsetsa kuti anthu akukhala moyo wopanda nkhawa, …
-
Lifestyle
Chiponde Beach Resort yakonza mwambo wapadera pofuna kubweletsa pamodzi anthu ochita malonda m’boma la Likoma.
M’mawu ake mkulu wamalo ogona alendo a Chiponde Beach Resort a Gedion Khuni ati mwambowu ubweletsa pamodzi anthu ochita malonda osiyanasiyana kuphatikizapo …
-
Lifestyle
Anthu okhala pa Chilumba cha Chizumulu apempha Boma kuti lipitilize mapulani omanga Jiti pachilumbachi.
Izi zadziwika pa mkumano omwe phungu wanyumba ya malamulo wa Likoma a Christopher Ashems Songwe anayitanitsa adindo osiyanasiyana kuphatikizapo mafumu lero pomwe …
-
Lifestyle
Ngati njira imodzi yochepetsa umbanda m’boma la Likoma Senior Chief Mkumpha yachititsa mkumano wa asodzi ochokela m’ma boma ena.
Polankhula pamsonkhanowu a Mathews Mwela anati anayitanitsa mkumanowu pomwe asodzi ochokera m’maboma ena akupita ku Likoma kukachita usodzi komanso bizinesi, asodziwa akuchokela …