A Chilambula alankhula izi lero atamaliza kupereka zikalata zawo zowayeneleza kudzapikisana nawo pachisankho chapa 16 September ngati mphungu pansi pa chipani cha …
Politics
-
-
Politics
Yemwe adzapikisane nawo pampando wa ukhansala muwodi ya Chizumulu North m’boma la Likoma ati ndiwokonzeka kutumikila anthu akuderali.
A Andrew Zex Msalowa omwe adzayimile chipani cha Malawi Congress Party MCP, anena izi lero pa Chizumulu Community ground pomwe amakhazikitsa mfundo …
-
Politics
A Philip Chika Chilambula omwe anagonja pachisankho chachipulura pa mpando wa ukhansala mchipani cha Democratic Progressive Party DPP, akuti adzapikisana nawo pampandowo ngati oyima pawokha.
A Chilambula alankhula ndi Likoma radio kuti sanali okhutila ndi chisankho chomwe chinachitika mwezi wa Epulu ndipo ati anthu asamakopeke ndi ndalama …
-
Politics
Phungu wa boma la Likoma a Christopher Ashems Songwe apeleka thandizo ku ofesi ya maphunziro m’bomali kuti lithandizile masewero osambila.
Phunguyu wapeleka thandizo la ndalama zokwana 1,000,000.00-kwacha lachisanu kudzera ku ofesi ya za masewero, District Education Sports Officer (DESO). Polandila thandizoli mkulu …
-
Politics
Gulu la Taskforce lomwe ndi nthambi ya chipani cha Malawi Congress Party m’boma la Likoma lapeleka Cement kuti amalizile nyumba ya chigayo.
Polankhula lachinayi pamwambo opeleka cement ku komiti yoyendetsa chigayochi, a Innocent Aponda omwe ndi mmodzi mwa guluri ati achita chidwi powona momwe …
-
Politics
Phungu waboma la Likoma a Christopher Ashems Songwe wati pali zokhoma zina zomwe zachititsa kuti munthawi yawo asakwanitse zina mwa zitukuko zomwe adalonjaza.
A Songwe anena izi lolemba pomwe anakonza mkumano wa adindo osiyanasiyana kuphatikizapo mafumu ndicholinga chowafotokozera zomwe achita kuchokera mchaka cha 2019. “Munthawi …