A Chilambula anena izi lamulungu kutsatila kufika kwa incinerator yi pa chipatala cha Chima m’bomali. “Kumbuyoku tikafuna kuwotcha zinthu zina tinkazitumiza ku …
Featured
-
-
Featured
Ofesi yowona za usodzi ku Likoma yati ndiyokondwa kuti tsopano asodzi ali ndi owaimira ku khonsolo.
Mkulu woyendetsa ntchito za usodzi m’boma la Likoma, Lonjezo Chikopa wati tsopano pakhala posavuta kuti asodzi azitha kutula nkhawa zawo komanso kudziwa …
-
Featured
Wapampando oyang’anila chitukuko chadera la kumwera kwa chilumba cha Likoma a Anson Putaputa ati akusowekera maphunziro kuti ayambe kugwira ntchito yawo mwaukadaulo.
A Putaputa anena izi kutsatila zomwe wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo yemwenso ndi phungu wa boma la Likoma a Charles Chilambula …
-
Featured
Wachiwiri kwa nduna ya zaumoyo yemwenso ndi phungu wa Likoma Islands Constituency olemekezeka a Charles Broomhead Chilambula ati boma ndilodzipereka kupititsa patsogolo ntchito zaumoyo.
A Chilambula amalankhula izi lero pamwambo otsegulira chipatala chaching’ono cha YoMa chomwe chamangidwa m’mudzi wa Yofu m’boma la Likoma. A Chilambula ati …
-
Featured
Khonsolo ya Likoma yalandira ma Computer asanu othandizira sukulu ya Likoma community technical college kuchokera ku Bungwe la TEVETA.
Polankhula lolemba pamwambo opeleka ma computer wa, mkulu woyendetsa ntchito za TEVETA m’chigawo chakumpoto a Joseph Chikopa ati ndicholinga chawo kuti Likoma …
-
Featured
Khansala Justina Phiri wa chigawo chakumpoto kwa Chilumba cha Chizumulu ndiyemwe wasankhidwa kukhala Wapampando wa Khonsolo ya Likoma.
Pa chisankho chomwe chachitika Lolemba motsogozedwa ndi bwana mkubwa wa khonsolo ya Likoma Abubakar Nkhoma, a Justina Phiri agonjetsa a Enerst Gulu …
-
Featured
‎kutsatila kutsegulira kwa sukulu pa 22 September chaka chino, gulu la achinyamata lochokera kwa a mfumu a Mani m’mudzi wa Mbungo lapeleka makope ndi zolembera kwa ana apasukulu ya mbungo m’boma la Likoma.‎‎
M,modzi mwa achinyamata omwe apelereka makopewa a Nick Mkuyamba ati cholinga chachikulu cha gulu lawo ndikupititsa patsogolo maphunziro musukulu za primary m’bomali.‎‎Nawo …
-
Vuto lakusowa kwa madzi a ukhondo lafika posauzana pa chilumba cha chizumulu m’boma la Likoma. Polankhula ndi Likoma Radio mkulu woyang’anira sikimu …
-
Featured
Sukulu ya Likoma Sekondale yalandila galimoto ya tsopano yomwe ikhale ikuchepetsa mavuto a mayendedwe.
Polandila galimotoyi lachinayi m’phunzitsi wamkulu wa pa sukukuyi a Jeremiah Mzumala ati akuthokoza boma kudzera ku nduna yoona za maphunziro a Madalitso …
-
Featured
Kuchedwetsa ntchito kwa kontilakitara kwapangitsa kuti ntchito yomanga chipatala chaching’ono cha YoMa healthy Post m’boma la Likoma chisathe munthawi yake.
Wachiwiri kwa wapampando wakomiti yoyang’anila chitukuko kuderali yemweso ndi wapampando wa chitukuko wa Yoma VDC a Aliston Katemetcha ati kontilakita yemwe akumanga …