Mwiniwake wa malo ogona alendo omwe akuwatcha kuti Mwayi Wanga Guest House m’boma la Likoma ati malowa awatsegulira pa 12 mwezi uno.
A Yamikani Mwambafula awuza Likoma Radio kuti pakadali pano chilichonse chokonzekera mwambowu chilimchimake ndipo ati patsikuli anthu ayembekezere kudzasangalatsidwa ndi oyimba osiyanasiyana…