Likoma FM
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • Likoma FM

    Apolisi m’boma la Likoma amanga a Charlse Banda, powaganizira kuti anachita chipongwe msungwana wazaka khumi.

    Mkulu woyang’anira nkhani za katemera wa Polio mdziko muno, a Blessing Nyirongo ati ali ndi chikhulupiliro kuti kampeni yopeleka katemera wamatendawa m’boma la Likoma ikhala yopambana.

    Wamkulu wa kampani ya Malawi Lake Services wati kukweza mitengo kwa sitima ya MV Ilala kupititsa patsogolo ntchito za kampaniyi.

    Apolisi m’boma la Likoma amanga a Charlse Banda, powaganizira kuti anachita chipongwe msungwana wazaka khumi.

    Chiletso BisweckApril 19, 2026021 views

    Malingana ndi mneneri wa Police ya Likoma a Andrew Kusimbwa ati kumangidwaku kwachitika pambuyo pa ntchito yomwe inachitika ndi a polisiwa. “A…

    Read more

    Mkulu woyang’anira nkhani za katemera wa Polio mdziko muno, a Blessing Nyirongo ati ali ndi chikhulupiliro kuti kampeni yopeleka katemera wamatendawa m’boma la Likoma ikhala yopambana.

    Oliver MalibisaMarch 22, 2026054 views

    A Nyirongo awuza Likoma Radio kuti kupeleka katemelayu kwatengera kupezeka kwa Polio munzinda wa Blantyre kotero a zaumoyo akangalika kupeleka katemelayu komanso…

    Read more

    Wamkulu wa kampani ya Malawi Lake Services wati kukweza mitengo kwa sitima ya MV Ilala kupititsa patsogolo ntchito za kampaniyi.

    Chiletso BisweckMarch 22, 2026042 views

    A Joseph Sheketani Banda alankhula izi lachinayi pamkumano omwe anakonzera atolankhani a m’boma la Likoma ndicholinga chowadziwitsa momwe kampaniyi imagwilira ntchito zake.…

    Read more

    Wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo yemwenso ndi phungu wa Likoma Islands Constituency a Charles Chilambula ati kubwera kwa incinerator m’boma la Likoma kupititsa patsogolo ntchito za umoyo.

    Chiletso BisweckMarch 1, 2026070 views

    A Chilambula anena izi lamulungu kutsatila kufika kwa incinerator yi pa chipatala cha Chima m’bomali. “Kumbuyoku tikafuna kuwotcha zinthu zina tinkazitumiza ku…

    Read more

    Ofesi yowona za usodzi ku Likoma yati ndiyokondwa kuti tsopano asodzi ali ndi owaimira ku khonsolo.

    Chiletso BisweckFebruary 20, 20260114 views

    Mkulu woyendetsa ntchito za usodzi m’boma la Likoma, Lonjezo Chikopa wati tsopano pakhala posavuta kuti asodzi azitha kutula nkhawa zawo komanso kudziwa…

    Read more

    Wapampando oyang’anila chitukuko chadera la kumwera kwa chilumba cha Likoma a Anson Putaputa ati akusowekera maphunziro kuti ayambe kugwira ntchito yawo mwaukadaulo.

    Chiletso BisweckFebruary 16, 2026086 views

    A Putaputa anena izi kutsatila zomwe wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo yemwenso ndi phungu wa boma la Likoma a Charles Chilambula…

    Read more

    Wachiwiri kwa nduna ya zaumoyo yemwenso ndi phungu wa Likoma Islands Constituency olemekezeka a Charles Broomhead Chilambula ati boma ndilodzipereka kupititsa patsogolo ntchito zaumoyo.

    Chiletso BisweckFebruary 5, 20260163 views

    A Chilambula amalankhula izi lero pamwambo otsegulira chipatala chaching’ono cha YoMa chomwe chamangidwa m’mudzi wa Yofu m’boma la Likoma. A Chilambula ati…

    Read more

    Atachita zii kwa zaka zinayi m’modzi mwa oyimba wapa chilumba cha Chizumulu, Memory Pondomali yemwe amatchuka ndi dzina lakuti Nyapondo wati akhala akutulutsa nyimbo yatsopano yomwe akuyitcha “Zani”.

    Chiletso BisweckJanuary 29, 20260174 views

    Nyapondo wati nyimboyi yomwe wajambula Video komanso audio zonse zitulutsidwa pa 1 February 2026, “panopa ndikhala okhazikika chifukwa ndinawoloka zomwe zakhala zikundifowoketsa…

    Read more

    Khonsolo ya Likoma yalandira ma Computer asanu othandizira sukulu ya Likoma community technical college kuchokera ku Bungwe la TEVETA.

    Chiletso BisweckDecember 16, 20250235 views

    Polankhula lolemba pamwambo opeleka ma computer wa, mkulu woyendetsa ntchito za TEVETA m’chigawo chakumpoto a Joseph Chikopa ati ndicholinga chawo kuti Likoma…

    Read more

    Khansala Justina Phiri wa chigawo chakumpoto kwa Chilumba cha Chizumulu ndiyemwe wasankhidwa kukhala Wapampando wa Khonsolo ya Likoma.

    Chiletso BisweckNovember 10, 202513285 views

    Pa chisankho chomwe chachitika Lolemba motsogozedwa ndi bwana mkubwa wa khonsolo ya Likoma Abubakar Nkhoma, a Justina Phiri agonjetsa a Enerst Gulu…

    Read more

    Posts navigation

    1 … 5
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top