Opindula ndi ndondomeko ya mtukula pakhomo m’boma la Likoma ati njira yatsopano yolandila ndalama kudzera pa phone ndiyodalilika.
Izi zadziwika Likoma radio itayendera ena mwa opindula ndi ndondomekoyi pa chilumba cha Chizumulu kufuna kunva momwe opindulawa ayilandilila njila yamakonoyi yomwe…