Kampani ya China Civil Engineering Construction kudzera mu unduna wa za mtengatenga ndi mtokoma yapereka ma life jacket 250 ku boma la Likoma.
M’mau ake m’modzi mwa akuluakulu oyang’anila za mayendedwe apa madzi omwe achokera ku nthambi ya Marine, Captain Peter Kajadu ati thandizoli ndilofunika…