Khansala Justina Phiri wa chigawo chakumpoto kwa Chilumba cha Chizumulu ndiyemwe wasankhidwa kukhala Wapampando wa Khonsolo ya Likoma.
Pa chisankho chomwe chachitika Lolemba motsogozedwa ndi bwana mkubwa wa khonsolo ya Likoma Abubakar Nkhoma, a Justina Phiri agonjetsa a Enerst Gulu…