Pofuna kupititsa patsogolo maphunziro mdziko muno wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo ndi ukhondo yemwenso ndi phungu wa pa zilumba za Likoma ndi Chizumulu wolemekezeka a Charles Chilambula apereka mabuku ku ofesi yoona za maphunziro m’boma la Likoma.
Mabukuwa ndi thandizo lochokera ku Malawi National Library Services ngati mayankho pazokambilana zimene mbali ziwirizi zinachita. Iwo awuza adindo kuti kubwera kwa…