Phungu waboma la Likoma a Christopher Ashems Songwe wati pali zokhoma zina zomwe zachititsa kuti munthawi yawo asakwanitse zina mwa zitukuko zomwe adalonjaza.
A Songwe anena izi lolemba pomwe anakonza mkumano wa adindo osiyanasiyana kuphatikizapo mafumu ndicholinga chowafotokozera zomwe achita kuchokera mchaka cha 2019. “Munthawi…