Ofesi yowona za usodzi ku Likoma yati ndiyokondwa kuti tsopano asodzi ali ndi owaimira ku khonsolo.
Mkulu woyendetsa ntchito za usodzi m’boma la Likoma, Lonjezo Chikopa wati tsopano pakhala posavuta kuti asodzi azitha kutula nkhawa zawo komanso kudziwa…