Vuto lakusowa kwa madzi a ukhondo lafika posauzana pa chilumba cha chizumulu m’boma la Likoma. Polankhula ndi Likoma Radio mkulu woyang’anira sikimu…
Vuto lakusowa kwa madzi a ukhondo lafika posauzana pa chilumba cha chizumulu m’boma la Likoma. Polankhula ndi Likoma Radio mkulu woyang’anira sikimu…
Polandila galimotoyi lachinayi m’phunzitsi wamkulu wa pa sukukuyi a Jeremiah Mzumala ati akuthokoza boma kudzera ku nduna yoona za maphunziro a Madalitso…
A Antonio Manda anena izi lero pamkumano omwe amakumana ndi atsogoleri oyendetsa masewero osayinasiyana m’bomali. M’mawu awo a Manda ati m’boma la…
A Chilambula alankhula izi lero atamaliza kupereka zikalata zawo zowayeneleza kudzapikisana nawo pachisankho chapa 16 September ngati mphungu pansi pa chipani cha…
M’mau ake m’modzi mwa akuluakulu oyang’anila za mayendedwe apa madzi omwe achokera ku nthambi ya Marine, Captain Peter Kajadu ati thandizoli ndilofunika…
A Andrew Zex Msalowa omwe adzayimile chipani cha Malawi Congress Party MCP, anena izi lero pa Chizumulu Community ground pomwe amakhazikitsa mfundo…
Wachiwiri kwa wapampando wakomiti yoyang’anila chitukuko kuderali yemweso ndi wapampando wa chitukuko wa Yoma VDC a Aliston Katemetcha ati kontilakita yemwe akumanga…
A Chilambula alankhula ndi Likoma radio kuti sanali okhutila ndi chisankho chomwe chinachitika mwezi wa Epulu ndipo ati anthu asamakopeke ndi ndalama…
Malingana ndi kalata yomwe bungweri ladatulutsa pa 9 Julayi ndipo wasaina ndi mneneri wa bungweri a Sangwani Mwafulirwa yati mwambo otsegulira nyengo…
Achakwera anena izi pamsonkhano wa achinyamata omwe ukuchitikira mu mzinda wa Lilongwe pamutu wakuti ‘Harnessing Youth Innovation for Economic Employment and Sustainable…