Pa chisankho chomwe chachitika Lolemba motsogozedwa ndi bwana mkubwa wa khonsolo ya Likoma Abubakar Nkhoma, a Justina Phiri agonjetsa a Enerst Gulu Banda omwe akhale wachiwiri kwa wapampando wa khonsoloyi.
Pamapeto amasankhowa a Justina alonjeza kuthandizira khonsolo ya Likoma pankhani za chitukuko powonetsetsa kuti ndondomeko zoyenera zikutsatidwa pachuma.
LikomaFM, OnlineNews.
13 comments