Pofuna kupititsa patsogolo ntchito za Maphunziro m’dziko muno, Nduna ya Maphunziro a Madalitso Kambauwa Wirima atsegulira ofesi ya aphunzitsi (TDC) pa chilumba cha Chizumulu m’boma la Likoma.
Polankhula la chiwiri pa Chilumba cha Chizumulu pamwambo otsegulira ofesiyi omwe unatsogozedwa ndi Phungu wa Likoma a Christopher Ashems Songwe, ndunayi yati…