Yemwe adzapikisane nawo pampando wa ukhansala muwodi ya Chizumulu North m’boma la Likoma ati ndiwokonzeka kutumikila anthu akuderali.
A Andrew Zex Msalowa omwe adzayimile chipani cha Malawi Congress Party MCP, anena izi lero pa Chizumulu Community ground pomwe amakhazikitsa mfundo…