Mulandu wayemwe akumuganizira kuti ndi m’modzi mwawoyendetsa Boat lomwe linachita ngozi ndikupha anthu nkhumi ndi modzi m’mawa wapa 12 April, 2025, m’boma la Likoma wayamba lero.
Malingana ndi His Worship Fordwatch Nyamazana Mkandawire wati mlanduwu ukuyembekezeka kupitilira lachisanu sabata ino. Naye otengera milandu ku bwalo lamilandu Sergeant Charles…