Khonsolo ya Boma la Likoma yayamba ntchito yomanga nyumba yosungilamo katundu wa ngozi zogwa mwadzidzi.
Ntchito yomanga nyumbayi yomwe imangidwe ku Ngani pansi pa CHAKO VDC yayambika lero ndipo igwilika kwa masiku 90. M’mawu awo nkulu oyang’anila…
Ntchito yomanga nyumbayi yomwe imangidwe ku Ngani pansi pa CHAKO VDC yayambika lero ndipo igwilika kwa masiku 90. M’mawu awo nkulu oyang’anila…
Rt.Rev. Fanuel Magangani wanena izi lamulungu lapitali pa St Peters Anglican Cathedral m’boma la likoma pamwambo osangalalira kuti Dioceses yi yakwanitsa zaka…
Phunguyu wapeleka thandizo la ndalama zokwana 1,000,000.00-kwacha lachisanu kudzera ku ofesi ya za masewero, District Education Sports Officer (DESO). Polandila thandizoli mkulu…
A Barnabas Sambamu anena izi lamulungu pomwe khonsolo ya Likoma inakonza masewelo ampira wamiyendo ndicholinga chakuti apeleke uthenga wamomwe porogalamuyi imayendela, pamutu…
Mkulu owona zachisankho m’boma la Likoma a Theophilus Msachi lero achititsa mkumano wa mafumu ndi atsogoleli azipembedzo pofuna kuwadziwitsa za ntchito yotsimikizila…
Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwanyengo yati nyengo ya Chiperoni ikuyembekezeka kuchepa mphanvu lero ndipo mawa m’madera ambiri kudzakhala kwa nyengo ya…
Polankhula la chiwiri pa Chilumba cha Chizumulu pamwambo otsegulira ofesiyi omwe unatsogozedwa ndi Phungu wa Likoma a Christopher Ashems Songwe, ndunayi yati…
A Songwe anena izi lolemba pomwe anakonza mkumano wa adindo osiyanasiyana kuphatikizapo mafumu ndicholinga chowafotokozera zomwe achita kuchokera mchaka cha 2019. “Munthawi…
Polankhula pamsonkhanowu a Mathews Mwela anati anayitanitsa mkumanowu pomwe asodzi ochokera m’maboma ena akupita ku Likoma kukachita usodzi komanso bizinesi, asodziwa akuchokela…
Madelawa ndi monga, Blantyre, Thyolo, Phalombe, Mangochi, Mwanza, Salima mwa ochepa chabe. Nthambiyi yati izi zikupereka chiyembekezo cha mvula ya mabingu m’maderawa…