Mkulu woyang’anira nkhani za katemera wa Polio mdziko muno, a Blessing Nyirongo ati ali ndi chikhulupiliro kuti kampeni yopeleka katemera wamatendawa m’boma la Likoma ikhala yopambana.
A Nyirongo awuza Likoma Radio kuti kupeleka katemelayu kwatengera kupezeka kwa Polio munzinda wa Blantyre kotero a zaumoyo akangalika kupeleka katemelayu komanso…