Pomwe dziko lino likukonzekera chisankho chapatatu bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electral Commission likupitiliza kudziwitsa adindo osiyanasiyana za ndondomeko yachisankho.
Mkulu owona zachisankho m’boma la Likoma a Theophilus Msachi lero achititsa mkumano wa mafumu ndi atsogoleli azipembedzo pofuna kuwadziwitsa za ntchito yotsimikizila…