Wachiwiri kwa nduna yoona za umoyo yemwenso ndi phungu wa Likoma Islands Constituency a Charles Chilambula ati kubwera kwa incinerator m’boma la Likoma kupititsa patsogolo ntchito za umoyo.
A Chilambula anena izi lamulungu kutsatila kufika kwa incinerator yi pa chipatala cha Chima m’bomali. “Kumbuyoku tikafuna kuwotcha zinthu zina tinkazitumiza ku…